Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usakhale ndi milungu ina iliyonse+ kupatulapo ine.* Deuteronomo 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anali kupereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sanaidziwe,+Milungu yatsopano yongobwera kumene,+Imene makolo anu akale sanaidziwe. Oweruza 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+
17 Iwo anali kupereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sanaidziwe,+Milungu yatsopano yongobwera kumene,+Imene makolo anu akale sanaidziwe.
8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+