Deuteronomo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usakhale ndi milungu ina iliyonse motsutsana ndi ine.+ 2 Mafumu 17:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 pamene Yehova anachita nawo pangano+ n’kuwalamula kuti: “Musamaope milungu ina.+ Musamaigwadire kapena kuitumikira kapenanso kupereka nsembe kwa iyo.+ Yeremiya 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo musatsatire milungu ina kuti muziitumikira ndi kuigwadira. Mukachita zimenezo mudzandikhumudwitsa chifukwa cha mafano anu amene mudzapanga, ndipo ineyo ndidzakugwetserani tsoka.’+
35 pamene Yehova anachita nawo pangano+ n’kuwalamula kuti: “Musamaope milungu ina.+ Musamaigwadire kapena kuitumikira kapenanso kupereka nsembe kwa iyo.+
6 Ndipo musatsatire milungu ina kuti muziitumikira ndi kuigwadira. Mukachita zimenezo mudzandikhumudwitsa chifukwa cha mafano anu amene mudzapanga, ndipo ineyo ndidzakugwetserani tsoka.’+