Ekisodo 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+ Deuteronomo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 (pakuti Yehova Mulungu wanu amene ali pakati panu ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi).+ Musatsatire milungu ina kuopera kuti mkwiyo wa Yehova Mulungu wanu ungakuyakireni,+ ndipo angakufafanizeni padziko lapansi.+ Yoswa 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mukasiya Yehova+ n’kuyamba kutumikira milungu yachilendo,+ iyenso adzakutembenukirani ndithu, n’kukuchitirani zoipa ndi kukufafanizani, pambuyo pokuchitirani zabwino.”+
5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+
15 (pakuti Yehova Mulungu wanu amene ali pakati panu ndi Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha basi).+ Musatsatire milungu ina kuopera kuti mkwiyo wa Yehova Mulungu wanu ungakuyakireni,+ ndipo angakufafanizeni padziko lapansi.+
20 Mukasiya Yehova+ n’kuyamba kutumikira milungu yachilendo,+ iyenso adzakutembenukirani ndithu, n’kukuchitirani zoipa ndi kukufafanizani, pambuyo pokuchitirani zabwino.”+