1 Mafumu 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+ 2 Mafumu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero Yehova anawakwiyira kwambiri+ Aisiraeli ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.+
34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+
18 Chotero Yehova anawakwiyira kwambiri+ Aisiraeli ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.+