Oweruza 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+
8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+