Yesaya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzaweruza achikulire pakati pa anthu ake ndi akalonga ake.+ “Inuyo mwatentha munda wa mpesa. Zinthu zimene zinabedwa kwa anthu ovutika zili m’nyumba zanu.+ Ezekieli 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu a m’dzikolo abera anthu pochita zachinyengo+ ndiponso zauchifwamba.+ Iwo akuzunza anthu osautsika ndi osauka.+ Abera mlendo pochita zachinyengo komanso zopanda chilungamo.’+ Hoseya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kutembererana,+ kuchita zachinyengo,+ kuphana,+ kuba,+ ndi chigololo+ zafala m’dzikoli, ndipo kukhetsa magazi kukuchitika motsatizanatsatizana.+ Mika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+
14 Yehova adzaweruza achikulire pakati pa anthu ake ndi akalonga ake.+ “Inuyo mwatentha munda wa mpesa. Zinthu zimene zinabedwa kwa anthu ovutika zili m’nyumba zanu.+
29 Anthu a m’dzikolo abera anthu pochita zachinyengo+ ndiponso zauchifwamba.+ Iwo akuzunza anthu osautsika ndi osauka.+ Abera mlendo pochita zachinyengo komanso zopanda chilungamo.’+
2 Kutembererana,+ kuchita zachinyengo,+ kuphana,+ kuba,+ ndi chigololo+ zafala m’dzikoli, ndipo kukhetsa magazi kukuchitika motsatizanatsatizana.+
2 Iwo alakalaka minda ya anthu ena ndipo ailanda.+ Alakalakanso nyumba za anthu ena n’kuzitenga kukhala zawo.+ Atenga mwachinyengo cholowa cha munthu ndi cha banja lake.+