Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Abusa ambiri+ awononga munda wanga wa mpesa.+ Apondaponda cholowa changa.+ Cholowa changa chosiririka+ achisandutsa bwinja moti palibe aliyense amene akukhalamo.

  • Luka 12:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Koma amene sanadziwe+ ndipo wachita zinthu zofunika kum’kwapula zikoti, adzam’kwapula zikoti zochepa.+ Inde, aliyense amene anapatsidwa zambiri, zambirinso zidzafunika kwa iye.+ Ndipo aliyense amene anthu anamuika kuyang’anira zinthu zochuluka, anthuwo adzafunanso zochuluka kwa iye.+

  • Yakobo 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Abale anga, pasakhale aphunzitsi ambiri pakati panu,+ podziwa kuti tidzalandira chiweruzo chachikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena