Salimo 80:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+ Yesaya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo munthu amene ndimamukonda. Imeneyi ndi nyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda, ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde m’mbali mwa phiri.
8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+
5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo munthu amene ndimamukonda. Imeneyi ndi nyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda, ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde m’mbali mwa phiri.