Salimo 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munapitikitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo m’malo mwawo munakhazikitsa anthu anu.+Munagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuipitikitsa.+ Salimo 78:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Chifukwa cha iwo anachotsa mitundu ina pang’onopang’ono m’dzikoli,+Ndipo anayesa dzikoli ndi kuligawa kwa iwo kukhala cholowa chawo,+Moti anachititsa mafuko a Isiraeli kukhala m’nyumba zawozawo.+
2 Munapitikitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo m’malo mwawo munakhazikitsa anthu anu.+Munagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuipitikitsa.+
55 Chifukwa cha iwo anachotsa mitundu ina pang’onopang’ono m’dzikoli,+Ndipo anayesa dzikoli ndi kuligawa kwa iwo kukhala cholowa chawo,+Moti anachititsa mafuko a Isiraeli kukhala m’nyumba zawozawo.+