Deuteronomo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,+Anaika malire a anthu+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+ Yoswa 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzikoli uligawe kwa mafuko 9 ndiponso kwa hafu ya fuko la Manase, kuti likhale cholowa chawo.”+ Salimo 136:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo dziko lawo analipereka kwa anthu ake kukhala cholowa:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,+Anaika malire a anthu+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+
21 Ndipo dziko lawo analipereka kwa anthu ake kukhala cholowa:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+