Ekisodo 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzawabweretsa ndi kuwakhazikitsa m’phiri limene ndi cholowa chanu.+Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukakhalemo,+ inu Yehova.Malo opatulika+ amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa. Salimo 80:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+
17 Mudzawabweretsa ndi kuwakhazikitsa m’phiri limene ndi cholowa chanu.+Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukakhalemo,+ inu Yehova.Malo opatulika+ amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa.
8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+