Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ine ndine Yehova wa makamu ndipo Isiraeli ndi munda wanga wa mpesa.+ Amuna a ku Yuda ndiwo mitengo ya mpesa imene ndinali kuikonda.+ Ine ndinali kuyembekezera chilungamo+ koma ndinaona anthu akuphwanya malamulo. Ndinali kuyembekezera zolungama koma ndinaona anthu akulira.”+

  • Yeremiya 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma ine ndinakubzala ngati mtengo wa mpesa wofiira, wabwino kwambiri.+ Mtengo wonsewo unali mbewu yeniyeni yabwino. Ndiye wandisinthira bwanji kukhala mphukira yachabechabe ya mtengo wa mpesa wachilendo?’+

  • Ezekieli 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Mayi anu+ anali ngati mtengo wa mpesa*+ wobzalidwa m’mphepete mwa madzi. Mtengowo unali kubereka zipatso ndipo unali ndi nthambi zambiri chifukwa unali pamadzi ambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena