Ekisodo 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mudzawabweretsa ndi kuwakhazikitsa m’phiri limene ndi cholowa chanu.+Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukakhalemo,+ inu Yehova.Malo opatulika+ amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa. Salimo 147:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova amasangalala ndi anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera kukoma mtima kwake kosatha.+ Salimo 149:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova amasangalala ndi anthu ake.+Iye amakongoletsa anthu ofatsa ndi chipulumutso.+
17 Mudzawabweretsa ndi kuwakhazikitsa m’phiri limene ndi cholowa chanu.+Malo okhazikika amene mwakonzeratu kuti mukakhalemo,+ inu Yehova.Malo opatulika+ amene manja anu, inu Yehova, anakhazikitsa.