Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Ndipo Yehova anandikwiyira chifukwa cha inu,+ kotero kuti analumbira kuti ndisawoloke Yorodano, kapena kulowa m’dziko labwino limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala cholowa chanu.+

  • Salimo 44:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Munapitikitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+

      Ndipo m’malo mwawo munakhazikitsa anthu anu.+

      Munagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuipitikitsa.+

  • Salimo 78:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Kenako anawalowetsa m’dziko lake lopatulika,+

      M’dera lamapiri ili limene dzanja lake lamanja linatenga.+

  • Salimo 80:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+

      Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena