Salimo 80:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munachititsa kuti mtengo wa mpesa+ uchoke mu Iguputo. Munathamangitsa mitundu ya anthu kuti mudzalemo mtengowo.+
8 Munachititsa kuti mtengo wa mpesa+ uchoke mu Iguputo. Munathamangitsa mitundu ya anthu kuti mudzalemo mtengowo.+