Numeri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine, polephera kundilemekeza+ pamaso pa ana a Isiraeli, simudzaulowetsa mpingowu m’dziko limene ndidzawapatse.”+ Deuteronomo 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo Yehova anapitiriza kundikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo sanandimvere. Motero Yehova anandiuza kuti, ‘Basi khala chete! Usatchulenso nkhani imeneyi kwa ine.
12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine, polephera kundilemekeza+ pamaso pa ana a Isiraeli, simudzaulowetsa mpingowu m’dziko limene ndidzawapatse.”+
26 Pamenepo Yehova anapitiriza kundikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo sanandimvere. Motero Yehova anandiuza kuti, ‘Basi khala chete! Usatchulenso nkhani imeneyi kwa ine.