Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete.

  • Numeri 27:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 chifukwa amuna inu munapandukira mawu anga m’chipululu cha Zini, pa nthawi imene khamu lija linakangana nanu.+ Munalephera kundilemekeza+ pa madzi amene anatuluka patsogolo pa khamulo, madzi a Meriba+ ku Kadesi,+ m’chipululu cha Zini.”+

  • Deuteronomo 32:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Izi zili choncho chifukwa anthu inu munachita mosakhulupirika kwa ine+ pakati pa ana a Isiraeli, kumadzi a pa Meriba+ ku Kadesi, m’chipululu cha Zini. Ndiponso chifukwa chakuti anthu inu simunandilemekeze pakati pa ana a Isiraeli.+

  • Yesaya 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova wa makamu ndi amene muyenera kumuona kuti ndi woyera,+ ndipo iyeyo ndi amene muyenera kumuopa.+ Iye ndi amene ayenera kukuchititsani kunjenjemera.”+

  • Chivumbulutso 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena