Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tumikirani Yehova mwamantha.+

      Kondwerani ndipo nthunthumirani.+

  • Salimo 76:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu ndinu wochititsa mantha,+

      Ndani angaime pamaso panu inu mutakwiya kwambiri?+

  • Yesaya 66:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+

  • Malaki 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Pangano limene ndinapangana naye linasunga moyo wake. Linamuthandizanso kukhala ndi moyo wamtendere.+ Chifukwa cha madalitso amenewa, anali kundiopa.+ Popeza kuti anali kulemekeza dzina langa, sankachita chilichonse chondikwiyitsa.+

  • Afilipi 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero, okondedwa anga, monga mmene mwakhalira omvera nthawi zonse,+ osati pokhapokha ine ndikakhalapo,* koma mofunitsitsa kwambiri tsopano pamene ine kulibe, pitirizani kukonza chipulumutso chanu, mwamantha+ ndi kunjenjemera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena