Salimo 95:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+ Salimo 99:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 99 Yehova wakhala mfumu.+ Mitundu ya anthu inthunthumire.+Iye wakhala pa akerubi.+ Ndipo dziko lapansi linjenjemere.+ Salimo 119:120 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+
95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+
99 Yehova wakhala mfumu.+ Mitundu ya anthu inthunthumire.+Iye wakhala pa akerubi.+ Ndipo dziko lapansi linjenjemere.+
120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+