Salimo 99:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 99 Yehova wakhala Mfumu.+ Mitundu ya anthu injenjemere. Iye wakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi.+ Dziko lapansi ligwedezeke. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 99:1 Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 91
99 Yehova wakhala Mfumu.+ Mitundu ya anthu injenjemere. Iye wakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi.+ Dziko lapansi ligwedezeke.