Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 14:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako anthu amene anali kutchire mumsasa ndi anthu onse kumudzi wa asilikaliwo anayamba kunjenjemera.+ Anthu olanda katundu+ nawonso anali kunjenjemera, ndipo nthaka inayamba kugwedezeka.+ Zimenezi zinali zochokera kwa Mulungu.+

  • Yobu 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Amachititsa dziko lapansi kunjenjemera pamalo ake,

      Mwakuti zipilala+ zake zimagwedezeka.

  • Salimo 82:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Milunguyo siikudziwa kanthu ndipo siikuzindikira.+

      Ikuyendayenda mu mdima,+

      Ndipo maziko onse a dziko lapansi agwedezeka.+

  • Ezekieli 38:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 ‘Ine ndidzalankhula mwaukali wanga+ woyaka moto komanso nditakwiya kwambiri.+ Ndithudi, pa tsikulo m’dziko la Isiraeli mudzachitika chivomezi chachikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena