Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamenepo phiri la Sinai linafuka utsi ponseponse,+ chifukwa chakuti Yehova anatsikira paphiripo m’moto.+ Utsi wakewo unali kukwera kumwamba ngati utsi wa uvuni,+ ndipo phiri lonse linali kunjenjemera kwambiri.+

  • Nahumu 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mapiri agwedezeka chifukwa cha iye ndipo zitunda zasungunuka.+

      Dziko lapansi, nthaka ndi zinthu zonse zokhala m’dzikomo zidzanjenjemera.+

  • Mateyu 27:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka, ndipo matanthwe anang’ambika.+

  • Machitidwe 16:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mwadzidzidzi panachitika chivomezi champhamvu, mpaka maziko a ndendeyo anagwedezeka. Nthawi yomweyo zitseko zonse zinatseguka, ndipo onse maunyolo awo anamasuka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena