Maliko 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamenepo nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati, kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Luka 23:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 popeza dzuwa linachita mdima. Pa nthawi imeneyi nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati+ kuchokera pamwamba mpaka pansi.
38 Pamenepo nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati, kuchokera pamwamba mpaka pansi.+
45 popeza dzuwa linachita mdima. Pa nthawi imeneyi nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati+ kuchokera pamwamba mpaka pansi.