Mateyu 27:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka, ndipo matanthwe anang’ambika.+ Luka 23:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 popeza dzuwa linachita mdima. Pa nthawi imeneyi nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati+ kuchokera pamwamba mpaka pansi.
51 Nthawi yomweyo nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Dziko lapansi linagwedezeka, ndipo matanthwe anang’ambika.+
45 popeza dzuwa linachita mdima. Pa nthawi imeneyi nsalu yotchinga+ ya m’nyumba yopatulika inang’ambika pakati+ kuchokera pamwamba mpaka pansi.