Ekisodo 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Upange nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pansaluyi upetepo akerubi.+ Aheberi 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+ Aheberi 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+
31 “Upange nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pansaluyi upetepo akerubi.+
3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+
20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+