Ekisodo 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Upange katani+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pakataniyi upetepo akerubi.
31 Upange katani+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pakataniyi upetepo akerubi.