1 Samueli 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anthu amene anali kutchire mumsasa ndi anthu onse kumudzi wa asilikaliwo anayamba kunjenjemera.+ Anthu olanda katundu+ nawonso anali kunjenjemera, ndipo nthaka inayamba kugwedezeka.+ Zimenezi zinali zochokera kwa Mulungu.+
15 Kenako anthu amene anali kutchire mumsasa ndi anthu onse kumudzi wa asilikaliwo anayamba kunjenjemera.+ Anthu olanda katundu+ nawonso anali kunjenjemera, ndipo nthaka inayamba kugwedezeka.+ Zimenezi zinali zochokera kwa Mulungu.+