Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Atatero anachoka, ndipo anthu a m’mizinda yowazungulira anagwidwa ndi mantha ochokera kwa Mulungu,+ moti sanatsatire ana a Yakobo kuti akawathire nkhondo.

  • Salimo 48:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Iwo anaona ndipo anadabwa.

      Anasokonezeka, moti anathawa mopanikizika kwambiri.+

  • Danieli 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pa nthawi imeneyo nkhope ya mfumuyo inasintha ndipo inachita mantha.+ Miyendo yake inafooka+ ndipo mawondo ake anayamba kunjenjemera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena