Salimo 69:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Maso awo achite mdima kuti asaone,+Ndipo chititsani miyendo* yawo kunjenjemera mosalekeza.+ Yesaya 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 N’chifukwa chake m’chiuno mwanga mwadzaza ululu woopsa.+ Zopweteka zandigwira, ngati zowawa za mkazi amene akubereka.+ Ndazunguzika moti sindikumva. Ndasokonezeka moti sindikuona.
3 N’chifukwa chake m’chiuno mwanga mwadzaza ululu woopsa.+ Zopweteka zandigwira, ngati zowawa za mkazi amene akubereka.+ Ndazunguzika moti sindikumva. Ndasokonezeka moti sindikuona.