Yesaya 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nʼchifukwa chake ndili pa ululu woopsa.*+ Zopweteka zandigwira,Ngati zowawa za mkazi amene akubereka. Ndili ndi nkhawa yaikulu moti sindikumva.Ndasokonezeka kwambiri moti sindikuona. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:3 Yesaya 1, ptsa. 217-218
3 Nʼchifukwa chake ndili pa ululu woopsa.*+ Zopweteka zandigwira,Ngati zowawa za mkazi amene akubereka. Ndili ndi nkhawa yaikulu moti sindikumva.Ndasokonezeka kwambiri moti sindikuona.