Yesaya 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 N’chifukwa chake m’chiuno mwanga mwadzaza ululu woopsa.+ Zopweteka zandigwira, ngati zowawa za mkazi amene akubereka.+ Ndazunguzika moti sindikumva. Ndasokonezeka moti sindikuona. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:3 Yesaya 1, ptsa. 217-218
3 N’chifukwa chake m’chiuno mwanga mwadzaza ululu woopsa.+ Zopweteka zandigwira, ngati zowawa za mkazi amene akubereka.+ Ndazunguzika moti sindikumva. Ndasokonezeka moti sindikuona.