Yeremiya 50:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Mfumu ya Babulo yamva za iwo,+ ndipo yataya mtima ndi kulefuka.+ Ikuda nkhawa ndipo ikumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+ 1 Atesalonika 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+
43 “Mfumu ya Babulo yamva za iwo,+ ndipo yataya mtima ndi kulefuka.+ Ikuda nkhawa ndipo ikumva zowawa ngati mkazi amene akubereka.+
3 Pamene azidzati:+ “Bata ndi mtendere!”+ chiwonongeko+ chodzidzimutsa chidzafika pa iwo nthawi yomweyo monga zowawa za pobereka za mkazi wapakati,+ ndipo sadzapulumuka.+