Yeremiya 49:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Damasiko wachita mantha. Watembenuka ndi kuthawa ndipo wapanikizika.+ Iye wagwidwa ndi nkhawa ndiponso zowawa za pobereka ngati zimene zimagwira mkazi amene akubereka.+
24 Damasiko wachita mantha. Watembenuka ndi kuthawa ndipo wapanikizika.+ Iye wagwidwa ndi nkhawa ndiponso zowawa za pobereka ngati zimene zimagwira mkazi amene akubereka.+