Yeremiya 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ife tamva uthenga wa zimenezi. Manja athu angoti lendee!+ Tagwidwa ndi nkhawa ndipo tikumva ululu ngati wa mkazi amene akubereka.+ Yeremiya 48:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Matauni adzalandidwa. Malo ake odalirika adzalandidwa. Pa tsikulo, mitima ya amuna amphamvu a ku Mowabu idzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.’”+
24 Ife tamva uthenga wa zimenezi. Manja athu angoti lendee!+ Tagwidwa ndi nkhawa ndipo tikumva ululu ngati wa mkazi amene akubereka.+
41 Matauni adzalandidwa. Malo ake odalirika adzalandidwa. Pa tsikulo, mitima ya amuna amphamvu a ku Mowabu idzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.’”+