Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno akakufunsa kuti, ‘N’chifukwa chiyani ukubuula?’+ Uwayankhe kuti, ‘N’chifukwa cha uthenga umene ndamva.’+ Pakuti uthengawo udzafika ndithu+ ndipo mtima wa munthu aliyense udzasungunuka ndi mantha.+ Anthu onse adzazizira nkhongono. Aliyense adzataya mtima ndipo mawondo onse adzachucha madzi.*+ ‘Uthengawo ufika ndithu+ ndipo zimene ukunena zidzachitikadi,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena