Ezekieli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi idzakwana, tsikulo lidzafika. Wogula asasangalale+ ndipo wogulitsa asalire, pakuti mkwiyo wa Mulungu wayakira khamu lonselo. 1 Petulo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira.+ Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+
12 Nthawi idzakwana, tsikulo lidzafika. Wogula asasangalale+ ndipo wogulitsa asalire, pakuti mkwiyo wa Mulungu wayakira khamu lonselo.
7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira.+ Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+