Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ine ndamva mawu ngati a mkazi amene akumva ululu. Ndamva ngati kubuula kwa mkazi amene akubereka mwana wake woyamba,+ koma ndi mawu a mwana wamkazi wa Ziyoni amene akupuma movutikira. Iye akutambasula manja ake+ ndi kulira kuti: “Tsoka ine, chifukwa ndatopa ndi anthu amene akufuna kundipha!”+

  • Yeremiya 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+

  • Yeremiya 49:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Damasiko wachita mantha. Watembenuka ndi kuthawa ndipo wapanikizika.+ Iye wagwidwa ndi nkhawa ndiponso zowawa za pobereka ngati zimene zimagwira mkazi amene akubereka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena