Yesaya 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero Yehova, amene anawombola Abulahamu, wanena izi kwa nyumba ya Yakobo:+ “Tsopano Yakobo sachita manyazi. Tsopano nkhope yake sikhala yakugwa,+
22 Chotero Yehova, amene anawombola Abulahamu, wanena izi kwa nyumba ya Yakobo:+ “Tsopano Yakobo sachita manyazi. Tsopano nkhope yake sikhala yakugwa,+