Yeremiya 45:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Iwe wanena kuti: “Tsoka ine!+ pakuti Yehova wawonjezera chisoni pa zopweteka zanga. Ndatopa ndi kuusa moyo* kwanga ndipo malo ampumulo sindikuwapeza.”’+ Ezekieli 23:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Khamu la anthulo lidzawaponya miyala+ ndi kuwapha ndi malupanga. Adzaphanso ana awo aamuna ndi aakazi+ ndi kutentha nyumba zawo.+
3 ‘Iwe wanena kuti: “Tsoka ine!+ pakuti Yehova wawonjezera chisoni pa zopweteka zanga. Ndatopa ndi kuusa moyo* kwanga ndipo malo ampumulo sindikuwapeza.”’+
47 Khamu la anthulo lidzawaponya miyala+ ndi kuwapha ndi malupanga. Adzaphanso ana awo aamuna ndi aakazi+ ndi kutentha nyumba zawo.+