-
Yeremiya 45:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 ‘Iwe wanena kuti: “Mayo ine! Yehova wawonjezera chisoni pa zopweteka zanga. Ndatopa ndi kubuula ndipo malo ampumulo sindikuwapeza.”’
-