Yeremiya 45:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Iwe wanena kuti: “Tsoka ine!+ pakuti Yehova wawonjezera chisoni pa zopweteka zanga. Ndatopa ndi kuusa moyo* kwanga ndipo malo ampumulo sindikuwapeza.”’+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:3 Yeremiya, ptsa. 103-105 Nsanja ya Olonda,8/15/2006, ptsa. 17-188/15/1997, tsa. 21
3 ‘Iwe wanena kuti: “Tsoka ine!+ pakuti Yehova wawonjezera chisoni pa zopweteka zanga. Ndatopa ndi kuusa moyo* kwanga ndipo malo ampumulo sindikuwapeza.”’+