Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+ Maliro 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ziyoni watambasula manja ake.+ Iye alibe womutonthoza.+Yehova walamula onse ozungulira Yakobo kuti akhale adani ake.+Yerusalemu wakhala chinthu chonyansa pakati pawo.+
15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+
17 Ziyoni watambasula manja ake.+ Iye alibe womutonthoza.+Yehova walamula onse ozungulira Yakobo kuti akhale adani ake.+Yerusalemu wakhala chinthu chonyansa pakati pawo.+