Mateyu 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwe popemphera, usanene zinthu mobwerezabwereza+ ngati mmene amachitira anthu a mitundu ina, chifukwa iwo amaganiza kuti Mulungu awamvera akanena mawu ambirimbiri.
7 Iwe popemphera, usanene zinthu mobwerezabwereza+ ngati mmene amachitira anthu a mitundu ina, chifukwa iwo amaganiza kuti Mulungu awamvera akanena mawu ambirimbiri.