Yesaya 51:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa ana onse amene iye anabereka, palibe ndi mmodzi yemwe+ amene anali kutsogolera mayiyo poyenda. Pa ana onse amene iye analera, palibe ndi mmodzi yemwe amene anagwira dzanja lake.+ Yeremiya 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Achigololo onse amene anali kukukonda kwambiri akuiwala.+ Iwo sakukufunafunanso. Ndakumenya ndi mkwapulo+ ngati mdani ndipo ndakulanga ngati munthu wankhanza+ chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako.+ Machimo ako achuluka kwambiri.+ Maliro 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zovala+ zake ndi zodetsedwa. Iye sanaganizire za tsogolo+ lake.Wagwa modabwitsa ndipo alibe womutonthoza.+Inu Yehova, onani kusautsika+ kwanga, pakuti mdani wanga akudzitukumula.+
18 Pa ana onse amene iye anabereka, palibe ndi mmodzi yemwe+ amene anali kutsogolera mayiyo poyenda. Pa ana onse amene iye analera, palibe ndi mmodzi yemwe amene anagwira dzanja lake.+
14 Achigololo onse amene anali kukukonda kwambiri akuiwala.+ Iwo sakukufunafunanso. Ndakumenya ndi mkwapulo+ ngati mdani ndipo ndakulanga ngati munthu wankhanza+ chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako.+ Machimo ako achuluka kwambiri.+
9 Zovala+ zake ndi zodetsedwa. Iye sanaganizire za tsogolo+ lake.Wagwa modabwitsa ndipo alibe womutonthoza.+Inu Yehova, onani kusautsika+ kwanga, pakuti mdani wanga akudzitukumula.+