Maliro 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+ Maliro 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndaitana anthu ondikonda kwambiri,+ koma anthuwo andichitira zachinyengo.Ansembe anga ndiponso akuluakulu atha+ mumzinda.Atha pamene anali kufunafuna chakudya choti adye kuti adzitsitsimutse.+
2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+
19 Ndaitana anthu ondikonda kwambiri,+ koma anthuwo andichitira zachinyengo.Ansembe anga ndiponso akuluakulu atha+ mumzinda.Atha pamene anali kufunafuna chakudya choti adye kuti adzitsitsimutse.+