Yeremiya 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yehova wanena kuti: ‘Kunena za aneneriwo amene akulosera m’dzina langa ngakhale kuti sindinawatume, amenenso akunena kuti lupanga kapena njala sizidzafika m’dziko lino, ndidzawawononga ndi lupanga ndiponso njala.+ Yeremiya 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Aneneri ndi ansembe, onse aipitsidwa+ ndipo m’nyumba mwanga ndapezamo zoipa zimene akuchita,”+ watero Yehova.
15 Choncho Yehova wanena kuti: ‘Kunena za aneneriwo amene akulosera m’dzina langa ngakhale kuti sindinawatume, amenenso akunena kuti lupanga kapena njala sizidzafika m’dziko lino, ndidzawawononga ndi lupanga ndiponso njala.+
11 “Aneneri ndi ansembe, onse aipitsidwa+ ndipo m’nyumba mwanga ndapezamo zoipa zimene akuchita,”+ watero Yehova.