Yeremiya 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Aneneri ndi ansembe, onse aipitsidwa.*+ Ndipo ngakhale mʼnyumba mwanga ndapezamo zoipa zimene akuchita,”+ akutero Yehova.
11 “Aneneri ndi ansembe, onse aipitsidwa.*+ Ndipo ngakhale mʼnyumba mwanga ndapezamo zoipa zimene akuchita,”+ akutero Yehova.