-
Ezekieli 13:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Dzanja langa lalimbana ndi aneneri amene akuona masomphenya abodza ndiponso amene akulosera zonama.+ Iwo sadzapitiriza kukhala m’gulu la anthu anga apamtima,+ komanso sadzalembedwa m’buku la mayina a anthu a nyumba ya Isiraeli.+ Sadzabwera kudziko la Isiraeli+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+
-