Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Komano ngati mukufuna kuwakhululukira tchimo lawo,+ . . . koma ngati simukufuna, ndifafanizeni+ chonde, m’buku lanu+ limene mwalemba.”

  • Nehemiya 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma Mulungu wanga anaika nzeru mumtima mwanga+ kuti ndisonkhanitse anthu olemekezeka, atsogoleri ndi anthu onse kuti alembetse mayina awo motsatira mzere wawo wobadwira.+ Ndiyeno ndinapeza buku la mndandanda wa mayina a mzere wobadwira+ wa anthu amene anabwera moyambirira kuchokera ku ukapolo. Ndinapeza kuti m’bukumo analembamo izi:

  • Salimo 69:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Afafanizidwe m’buku la anthu amoyo,+

      Ndipo iwo asalembedwe m’bukumo pamodzi ndi anthu olungama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena