1 Mbiri 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli onse analembedwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo+ m’Buku la Mafumu a Isiraeli. Ayuda anatengedwa kupita ku ukapolo+ ku Babulo chifukwa cha kusakhulupirika kwawo. Ezara 2:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Amenewa ndiwo anayang’ana mayina awo m’kaundula kuti atsimikizire anthu onse za mzere wawo wobadwira koma sanapezekemo. Zitatero anawaletsa kuti asatumikire monga ansembe chifukwa anali oipitsidwa.+
9 Aisiraeli onse analembedwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo+ m’Buku la Mafumu a Isiraeli. Ayuda anatengedwa kupita ku ukapolo+ ku Babulo chifukwa cha kusakhulupirika kwawo.
62 Amenewa ndiwo anayang’ana mayina awo m’kaundula kuti atsimikizire anthu onse za mzere wawo wobadwira koma sanapezekemo. Zitatero anawaletsa kuti asatumikire monga ansembe chifukwa anali oipitsidwa.+